This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Woyendetsa njinga yamoto yemwe ananyamula zigubu zamafuta a galimoto, wafa atagwa ndikuyaka moto pomwe amathamangitsidwa ndi a polisi. Malingana ndi yemwe tawona pa tsamba la Facebook, izi zachitika pa Kanengo mu mzinda wa Lilongwe. Mu kanemayu mukuveka mau a yemwe amajambula ndipo wafotokoza kuti wanjingayu amathawa galimoto yapolisi yomwe imamuthangitsa, koma anakagwera kutchire komwe moto […]
Read the full article and more Malawi news at Wanjinga wafa pothawitsa mafuta kwa apolisi">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
